It is very hot
Kukutentha kwambiri
While/when/where
Pamene
Sit down
Khala
Sleep/lie down
Gona
There is
Kuli/pali/muli
There is no water
Palibe madzi
They don’t know
Sakudziwa
Early in the morning
M’mawa kwambiri
Speak
Yankhula
Say
Nena
Narrate/explain
Kamba
When
Liti
Who
Ndani
What
Chani
Where
Kuti
Forget
Iwala
Sell
Gulitsa
Drive
Yendetsa
Luggage/purse/wallet
Chikwama
Big bag for maize/wheat/rice
Thumba
I am going to forget
Ndiwala
I have forgotten
Ndaiwala