lächeln
mwetula
lachen (über etw.)
seka
lahmen
lumula
Lampe
nyale (5)
Land
dziko (4)
Landkarte
map (4)
ländlich
a kumudzi
Landschaft
chilengedwe (3)
Landwirtschaft
ulimi (6)
lang (Entfernung)
tali
lang(e) Zeit
nthawi yaitali
langsam
mosafulumira, pang’ono pang’ono
langweilig
a boa
Lärm
phokoso (5)
laufen, rennen
thamanga
laut
a phokoso
leben
khala (ndi moyo)
Leben
moyo (5)
Lebensmittel
chakudya (3)
lecker
koma
ledig
o sakwatira
leer sein
mulibe kanthu
legen
ika
Lehrer(in)
mphunzitsi (1)