Ndi zimene ndimafuna
That’s what I need
Ndili nazo
I have it
Tinakusowani
We missed you
Lolemba si tsiku labwino
Monday isn’t a good day
Ndikuganiza kuti
I think that
Kudzewa nsomba
To fish fish
Mwakonzeka?
Are you ready?
Sindikukumbikira zimenezo.
I can’t remember that.