Kodi
General Word to introduce a question
Bwanji?
How
Ndani?
Who?
Liti?
When?
Nthawi Yanji?
What time?
Chiyani/chani?
What?
Kuti?
Where?
Chifukwa chiyani?
Why?
Kaya
What about?
Nanga?
What about?
-ngati
How many? or How much?
-nji?
What kind?
-tani?
What kind?
Nthawi yayitali bwanji?
How long?
Njiri iti?
Which way?
Ndalama zingati?
How much money?